Teeth whitening powder

Teeth whitening powder

Active
MK 15,000
Zomba, • Timapezeka pa kips
• Ad #MP5593
Condition: New
20
Views
0
Reviews
0.0
Rating
SK
Skinluxe Store
Contact Verified ID Verified
Member since Oct 2026 • 18 active listings
0.0 (0 reviews)
Seller Trust
0
Vouches
0.0
Rating
0%
5-Star

Details

  • Category: Fashion & Beauty
  • Condition: New
  • Price: MK 15,000
  • Negotiable: No
  • Location: Zomba, Southern (Timapezeka pa kips)

Description

Kuyeretsa mano othimbilira ndi *TOOTH WHITENING POWDER* Powder uyu amayeretsa mano othimbilira kwa Mankhwala amenewa ndi opangidwa kuchokera ku zachilengedwe. *Ntchito zake*; 1. Kuchotsa zothimbilira zonse zammano zokuda, zayellow, zodza kaamba ka kutsuta fodya ndi zokumwa zina komanso zothimbiliritsa mano za mtundu ulionse. 2. Kuyeretsa mano othimbilira mpaka kale. 3. Kutsamalira mkamwa kuthana ndi fungo loyipa la mkamwa lochokera mmano. 4. Kulimbitsa mano. *Kagwiritsidwe ntchito* 1. Nyowetsani toothbrush yanu 2. Ikaponi powder 3. Chukuchani mano kwa 2 to 3 minutes Tsukani mkamwa ndi madzi. *Akuyenera kugwiritsa ntchito* Munthu aliyense kuyambila dzaka Tsopano mwathana ndi mavuto akuthimbilira kwa mano chifukwa cha zakudya, zakumwa, fodya komanso mowa!!