MALONDA A MALO PA MZIMBA BOMA
ActiveMK 3,700,000
Condition: Good
Price Negotiable
44
Views
0
Reviews
0.0
Rating
DA
Davis Nyirenda
Contact Verified
ID Verified
Member since Mar 2026 •
2 active listings
Seller Trust
0
Vouches
0.0
Rating
0%
5-Star
More from Davis Nyirenda
Details
- Category: Land for Sale
- Condition: Good
- Price: MK 3,700,000
- Negotiable: Yes
- Location: Mzimba, Northern (Chanthomba)
Description
PLOT LIJA LATSIKA MTENGO - MZIMBA BOMA - Pali plot ili la malonda, size 22 m by 27 metres ku dela la Kafoteka. zinangoyang'anizana ndi Rada Academy komanso Thandeka Pvt Sec ndi Z.Mtika Warehouse. - Lili pa mtunda wa 1 km kufika mu tar road. Mpofika ma galimoto, madzi pafupinso, Magesi pafupi, palinso ma kotaz osamaliza atatu (ofuna kukhoma) - MTENGO K3.7 million (kukambilana kuliponso) - TIPEZENI PA WHATSAPP A MA NUMBER AWA * +27649745660 * +265982972703 NB Malonda awa akutsatsidwa ndi mwini Malo. osati agent🙏